Gå direkte til innholdet
Nditha Kuwerenga Baibulo Langa
Spar

Nditha Kuwerenga Baibulo Langa

Forfatter:
pocket, 2012
Engelsk
Thandizani ana anu kukhala odzidalira powerenga okha Baibulo Aloreni kuwerenga okha nkhani zosangalatsa zosiyanasiyana za m'baibulo pa nthawi imene akufuna kutero. Mwakutero, adzakhala ndi lusa lomvetsa zinthu pawokha mwachangu ndi kuzigwilitsa bwino ntchito chomwe ndi chuma chokhazikika. Lolani kuti, chikondi cha Mulungu chomwe ndi chopanda malire, chiwalire pa miyoyo ya ana anu.
ISBN
9781291113198
Språk
Engelsk
Vekt
268 gram
Utgivelsesdato
6.10.2012
Forlag
Lulu.com
Antall sider
108