Siirry suoraan sisältöön
  1. Kirjat
  2. Lasten- ja nuortenkirjat
  3. 3-6 vuotiaille

Mphaka Wamphamvu Zochiritsa

16,40 €

Celesse, the healer cat, is a highly respected member of the neighborhood. As the mistress's favorite cat, she spends lazy days in the warmth of the house.
One snowy night a mother hare rushes in, desperate for help. Reluctantly, the healer cat travels with her through a nighttime snowstorm and biting cold winds. In a dark forest, Celesse comes face-to-face with a scary surprise and is forced to gather her powers for the first time in a while.
---
Mphaka winawake dzina lake Silese, ankatha kuchiritsa matenda osiyanasiyana. Chifukwa cha mphatso yakeyi, mphakayu ankalemekezedwa kwambiri m'dera lonse limene amakhala. Nawonso adona a m'nyumba imene Silese ankakhala ankam'konda kwambiri poyerekeza ndi ziweto zonse zimene anali nazo panyumbapo.
Tsiku lina, mwana wa kalulu anadwala mwakayakaya. Mayi wake ataona kukula kwa matendawo, anapita kukapempha mphaka wochiritsa uja kuti abwere adzathandize mwanayo. Koma mphakayo sankafuna kumuthandiza chifukwa kunja kunali kutada komanso kukuzizira kwambiri. Kaluluyo ataumirirabe, mphakayo analolera n'kunyamuka. Ali m'njira, anakumana ndi nkhandwe yoopsa kwambiri. Koma Silese anakwanitsa kulimbana nayo ndipo anapitiriza ulendo wawo.
Kenako anafika kunyumba kwa kaluluyo ndipo anathandiza mwana wodwala uja. Kutacha m'mawa, dzuwa linatuluka ndipo kunja kunayamba kufunda. Silese anauyamba ulendo wobwerera kwawo ali ndi chimwemwe chodzadza tsaya.

Alaotsikko
Chichewa Edition of The Healer Cat
Kirjailija
Tuula Pere
Kuvittaja
Klaudia Bezak
Kääntäjä
Symon Simbotah
ISBN
9789523571617
Kieli
njandža
Paino
127 grammaa
Julkaisupäivä
1.9.2021
Kustantaja
WickWick
Sivumäärä
40